Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Hoseya 10:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo misanje ya Aveni, ndiyo cimo la Israyeli, idzaonongeka; minga ndi mitungwi idzamera pa maguwa ao a nsembe; ndipo adzati kwa mapiri, Tiphimbeni; ndi kwa zitunda, Tigwereni.

Werengani mutu wathunthu Hoseya 10

Onani Hoseya 10:8 nkhani