Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Hoseya 10:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Efraimu ndiye ng'ombe yaikazi yaing'ono, yozereweredwa, yokonda kupuntha tirigu; koma ndapita pa khosi lace lokoma; ndidzamsenzetsa Efraimu goli; Yuda adzalima, Yakobo adzaphwanya cibuluma cace.

Werengani mutu wathunthu Hoseya 10

Onani Hoseya 10:11 nkhani