Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Habakuku 2:19-20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

19. Tsoka iye wakunena kwa mtengo, Galamuka; ndi kwa mwala wosalankhula, Nyamuka Kodi ici ciphunzitsa? Taona cakutidwa ndi golidi ndi siliva, ndi m'kati mwace mulibe mpweya konse.

20. Koma Yehova ali m'Kacisi wace wopatulika; dziko lonse lapansi ale, cete pamaso pace.

Werengani mutu wathunthu Habakuku 2