Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Habakuku 1:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Inu wa maso osalakwa, osapenya coipa, osakhoza kupenyerera cobvuta, mupenyereranji iwo akucita mocenjerera, ndi kukhala cete pamene woipa ammeza munthu wolungama woposa iye mwini;

Werengani mutu wathunthu Habakuku 1

Onani Habakuku 1:13 nkhani