Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 9:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Semu ndi Yafeti ndipo anatenga copfunda, naciika pa mapewa ao a onse awiri, nayenda cambuyo, napfunditsa umarisece wa atate wao: nkhope zao zinali cambuyo, osaona umarisece wa atate ao.

Werengani mutu wathunthu Genesis 9

Onani Genesis 9:23 nkhani