Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 9:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo ndidzakumbukira pangano langa limene liri ndi Ine ndi inu, ndi zamoyo zonse zokhala ndi moyo; ndipo madzi sadzakhalanso konse cigumula cakuononga zamoyo zonse.

Werengani mutu wathunthu Genesis 9

Onani Genesis 9:15 nkhani