Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 8:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

koma njiwayo siinapeza popondapo phazi lace, nibwera kwa iye kucingalawako, pakuti madzi analipo pa dziko lonse lapansi; ndipo anaturutsa dzanja lace, naitenga, nailowetsa kwa iye m'cingalawamo.

Werengani mutu wathunthu Genesis 8

Onani Genesis 8:9 nkhani