Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 8:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Turutsa pamodzi ndi iwe zamoyo zonse ziti ndi iwe za nyama zonse, zouluka, ndi zinyama, ndi zokwawa zonse zakukwawa pa dziko lapansi; kuti ziswane pa dziko lapansi, zibalane, zicuruke pa dziko lapansi.

Werengani mutu wathunthu Genesis 8

Onani Genesis 8:17 nkhani