Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 6:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pa dziko lapansi panali anthu akurukuru masiku omwewo ndiponso pambuyo pace, ana amuna a Mulungu atalowa kwa ana akazi a anthu, ndipo anabalira iwo ana, amenewo ndiwo anthu amphamvu akalekale, anthu omveka.

Werengani mutu wathunthu Genesis 6

Onani Genesis 6:4 nkhani