Ndine, taonani, ndipo Ine ndidzadzetsa cigumula ca madzi pa dziko lapansi, kuti cionooge zamoyo zonse, m'mene muli mpweya wa moyo pansi pa thambo; zinthu zonse za m'dziko lapansi zidzafa.