Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 50:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yosefe anapita kukaika atate wace; ndipo anakwera pamodzi ndi akapolo onse a Farao, ndi akuru a pa mbumba yace, ndi akuru onse a m'dziko la Aigupto,

Werengani mutu wathunthu Genesis 50

Onani Genesis 50:7 nkhani