Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 50:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yosefe anakhala m'Aigupto, iye, ndi mbumba ya atate wace; ndipo Yosefe anakhala ndi movo zaka zana limodzi ndi khumi.

Werengani mutu wathunthu Genesis 50

Onani Genesis 50:22 nkhani