Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 50:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene abale ace a Yosefe anaona kuti atate wao anafa, anati, Kapena Yosefe adzatida ife, ndipo adzatibwezera ife zoipa zonse tidamcitira iye.

Werengani mutu wathunthu Genesis 50

Onani Genesis 50:15 nkhani