Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 5:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ili ndi buku la mibadwo ya Adamu. Tsiku lomwe Mulungu analenga munthu anamlenga m'cifanizo ca Mulungu;

2. anawalenga iwo mwamuna ndi mkazi, nawadalitsa iwo nacha mtundu wao anthu, tsiku lomwe anawalenga iwo.

Werengani mutu wathunthu Genesis 5