Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 49:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo analangiza iwo nati kwa iwo, Ine nditi ndisonkhanizidwe kwa anthu a mtundu wanga; mundiike ine pamodzi ndi makolo anga m'phanga liri m'munda wa Efroni Mhiti,

Werengani mutu wathunthu Genesis 49

Onani Genesis 49:29 nkhani