Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 48:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsopano ana ako amuna awiri, amene anakubadwira iwe m'dziko la Aigupto, ndisanadze kwa iwe ku Aigupto, ndiwo anga; Efraimu ndi Manase, monga Rubeni ndi Simeoni, ndiwo anga.

Werengani mutu wathunthu Genesis 48

Onani Genesis 48:5 nkhani