Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 47:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

dziko la Aigupto liri pamaso pako: uwakhazike atate wako ndi abale ako pa dera lokometsetsa la dziko; akhale m'dziko la Goseni; ndipo ngati udziwa anthu anzeru a mwa iwo, uwaike iwo ayang'anire ng'ombe zanga.

Werengani mutu wathunthu Genesis 47

Onani Genesis 47:6 nkhani