Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 47:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati kwa Farao, Tafika kuti tikhale m'dzikomo; popeza palibe podyetsa zoweta za akapolo anu; pakuti njala yakula m'dziko la Kanani. Mulole tsopano akapolo anu akhale m'dziko la Goseni.

Werengani mutu wathunthu Genesis 47

Onani Genesis 47:4 nkhani