Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 47:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yosefe anasonkhanitsa ndalama zonse anazipeza m'dziko la Aigupto ndi m'dziko la Kanani, za tirigu amene anagula; ndipo Yosefe anapereka ndalama ku nyumba ya Farao.

Werengani mutu wathunthu Genesis 47

Onani Genesis 47:14 nkhani