Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 47:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yosefe analowa nauza Farao nati, Atate wanga ndi abale anga, ndi nkhosa zao ndi ng'ombe zao, ndi zonse ali nazo, anacokera ku dziko la Kanani; ndipo, taonani, ali m'dziko la Goseni.

Werengani mutu wathunthu Genesis 47

Onani Genesis 47:1 nkhani