Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 46:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yakobo anacoka ku Beereseba, ndipo ana amuna a Israyeli anamnyamula Yakobo atate wao, ndi ana ao ang'ono, ndi akazi ao, m'magareta amene Farao anatumiza kuti amnyamule iye,

Werengani mutu wathunthu Genesis 46

Onani Genesis 46:5 nkhani