Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 46:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Amenewo ndi ana amuna a Leya, amene anambalira Yakobo m'Padanaramu, pamodzi ndi mwana wamkazi wace Dina; ana amuna ndi akazi onse: ndiwo anthu makumi atatu kudza atatu.

Werengani mutu wathunthu Genesis 46

Onani Genesis 46:15 nkhani