Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 46:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo Israyeli anamuka ulendo wace ndi zonse anali nazo, nafika ku Beereseba, napereka nsembe kwa Mulungu wa Isake atate wace.

2. Ndipo Mulungu ananena kwa Israyeli, m'masomphenya a usiku, nati, Yakobo, Yakobo.

Werengani mutu wathunthu Genesis 46