Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 45:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mulungu anatumiza ine patsogolo panu kuti ndikhazike inu mutsale m'dziko lapansi, ndi kusunga inu amoyo ndi cipulumutso cacikuru.

Werengani mutu wathunthu Genesis 45

Onani Genesis 45:7 nkhani