Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 45:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yosefe anati kwa abale ace, Muyandikiretu kwa ine; nayandikira. Ndipo iye anati, Ine ndine Yosefe mbale wanu, ine ndemwe munandigulitsa ndilowe m'Aigupto.

Werengani mutu wathunthu Genesis 45

Onani Genesis 45:4 nkhani