Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 45:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Onse anawapatsa yense zobvala zopindula; koma Benjamini anampatsa ndalama zasiliva mazana atatu ndi zobvala zopindula zisanu.

Werengani mutu wathunthu Genesis 45

Onani Genesis 45:22 nkhani