Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 44:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tinati kwa mbuyanga, Tiri ndi atate, munthu wokalamba, ndi mwana wa ukalamba wace wamng'ono; mbale wace wafa, ndipo iye yekha watsala wa amace, ndipo atate wace amkonda iye.

Werengani mutu wathunthu Genesis 44

Onani Genesis 44:20 nkhani