Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 44:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndico Yuda anati, Kodi tidzati bwanji kwa mbuyanga? kodi tidzanenanji? kapena tidzawiringula ife bwanji? Mulungu wapeza mphulupulu ya akapolo anu; taonani, tiri akapolo a mbuyanga, ife ndi iye amene anampeza naco cikho m'dzanja lace.

Werengani mutu wathunthu Genesis 44

Onani Genesis 44:16 nkhani