Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 43:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yosefe anafulumira, cifukwa mtima wace unakhumbitsa mphwace, ndipo mafuna polirira; nalowa m'cipinda ace naliramo.

Werengani mutu wathunthu Genesis 43

Onani Genesis 43:30 nkhani