Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 43:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo panali pamene ife tinafika padgono, tinamasula matumba athu, ndipo taonani ndalama za yense zinali kukamwa kwa thumba lace, ndalama zathu mkulemera kwace; ndipo tabwera nazo m'manja mwathu.

Werengani mutu wathunthu Genesis 43

Onani Genesis 43:21 nkhani