Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 43:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Israyeli atate wao anati kwa iwo, Ngati comweco tsopano citani ici: tengani zipatso za m'dziko muno m'zotengera zanu, mumtengere munthu uja mphatso, mafuta a mankhwala pang'ono, ndi uci pang'ono, zonunkhira ndi mure, ndi mfula, ndi katungurume;

Werengani mutu wathunthu Genesis 43

Onani Genesis 43:11 nkhani