Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 42:38 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye anati, Mwana wanga sadzatsikira ndi inu, cifukwa kuti mkuru wace wafa, ndipo watsala iye yekha; ngati coipa cikamgwera iye m'njira m'mene mupitamo, inu mudzatsitsira ndi cisoni imvi zanga kumanda.

Werengani mutu wathunthu Genesis 42

Onani Genesis 42:38 nkhani