Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 41:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali m'mamawa mtima wace unabvutidwa; ndipo anatumiza naitana amatsenga onse a m'Aigupto, ndi anzeru onse a momwemo: ndipo Farao anafotokozera iwo loto lace; koma panalibe mmodzi anakhoza kuwamasulira iwo kwa Farao.

Werengani mutu wathunthu Genesis 41

Onani Genesis 41:8 nkhani