Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 41:48 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anasonkhanitsa cakudya conse ca zaka zisanu ndi ziwiri cimene cinali m'dziko la Aigupto, nasunga cakudyaco m'midzi; cakudya ca m'minda, yozinga midzi yonse, anacisunga m'menemo.

Werengani mutu wathunthu Genesis 41

Onani Genesis 41:48 nkhani