Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 41:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ng'ombe zazikazi zisanu ndi ziwiri zoonda ndi za maonekedwe oipa zinaturuka pambuyo pao ndizo zaka zisanu ndi ziwiri, ndiponso ngala zisanu ndi ziwiri zopanda kanthu zopsyerera ndi mphepo ya kum'mawa, ndizo zaka zisanu ndi ziwiri za njala.

Werengani mutu wathunthu Genesis 41

Onani Genesis 41:27 nkhani