Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 40:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamene wophika mkate anaona kuti mmasuliro wace unali wabwino, iye anati kwa Yosefe, Inenso ndinalimkulota, ndipo, taonani, malicero atatu a mikate yoyera anali pamtu panga;

Werengani mutu wathunthu Genesis 40

Onani Genesis 40:16 nkhani