Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 4:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ukacita zabwino, sudzalandiridwa kodi? Ukaleka kucita zabwino, ucimo ubwatama pakhomo: kwa iwe kudzakhala kulakalaka kwace, ndipo iwe udzamlamulira iye.

Werengani mutu wathunthu Genesis 4

Onani Genesis 4:7 nkhani