Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 4:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Kaini anamdziwa mkazi wace; ndipo anatenga pakati, nabala Enoke: ndipo anamanga mudzi, naucha dzina lace la mudziwo monga dzina la mwana wace, Enoke.

Werengani mutu wathunthu Genesis 4

Onani Genesis 4:17 nkhani