Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 39:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

mulibe wina m'nyumba wamkuru ndine; ndipo sanandikaniza ine kanthu, koma iwe, cifukwa kuti uli mkazi wace: nanga ndikacita coipa cacikuru ici bwanji ndi kucimwira Mulungu?

Werengani mutu wathunthu Genesis 39

Onani Genesis 39:9 nkhani