Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 39:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Woyang'anira m'kaidi sanayang'anira kanthu kali konse kamene kanali m'manja a Yosefe, cifukwa Yehova anali ndi iye; ndipo zimene anazicita, Yehova anazipindulitsa.

Werengani mutu wathunthu Genesis 39

Onani Genesis 39:23 nkhani