Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 38:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali itapita miyezi itatu, anamuuza Yuda kuti, Tamara mpongozi wako wacita cigololo, ndiponso taonani, ali ndi pakati ndi cigololoco. Ndipo Yuda anati, Mturutse iye kuti amponye pamoto.

Werengani mutu wathunthu Genesis 38

Onani Genesis 38:24 nkhani