Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 38:2-4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

2. Ndipo Yuda anaona kumeneko mwana wamkazi wa Mkanani dzina lace Sua: ndipo anamtenga, nalowa kwa iye.

3. Ndipo anatenga pakati, nabala mwana wamwamuna, namucha dzina lace Eri.

4. Ndipo anatenganso pakati, nabala mwana wamwamuna, namucha dzina lace Onani.

Werengani mutu wathunthu Genesis 38