Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 38:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye anati, Cikole canji ndidzakupatsa iwe? Ndipo mkazi anati, Mphete yako, ndi cingwe cako, ndi ndodo iri m'dzanja lako. Ndipo anampatsa izo, nalowana naye, ndipo mkazi anatenga pakati ndi iye.

Werengani mutu wathunthu Genesis 38

Onani Genesis 38:18 nkhani