Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 38:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo panali nthawi yomweyo, kuti Yuda anatsikira kwa abale ace nalowa kwa M-adulami, dzina lace Hira.

2. Ndipo Yuda anaona kumeneko mwana wamkazi wa Mkanani dzina lace Sua: ndipo anamtenga, nalowa kwa iye.

Werengani mutu wathunthu Genesis 38