Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 37:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iwo anakhala pansi kuti adye cakudya; ndipo anatukula maso ao, nayang'ana, ndipo taonani, ulendo wa Aismayeli anacokera ku Gileadi ndi ngamila zao, zilinkunyamula zonunkhira ndi mafuta amankhwala ndi libano alinkumuka kutsikira nazo ku Aigupto.

Werengani mutu wathunthu Genesis 37

Onani Genesis 37:25 nkhani