Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 37:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Rubeni anati kwa iwo, Musakhetse mwazi; mponyeni iye m'dzenjemo m'cipululu muno, koma musamsamulire iye manja: kuti ampulumutse iye ra'manja mwao, ambwezenso kwa atate wace.

Werengani mutu wathunthu Genesis 37

Onani Genesis 37:22 nkhani