Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 37:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Munthuyo ndipo anati, Anacoka pano; pakuti ndinamva alinkuti, Timuke ku Dotana. Yosefe ndipo anatsata abale ace, nawapeza ali ku Dotana.

Werengani mutu wathunthu Genesis 37

Onani Genesis 37:17 nkhani