Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 37:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati kwa iye, Pita tsopano, nukaone ngati abale ako ali bwino, ndi ngati zoweta ziri bwino; nundibwezere ine mau. Ndipo anamtuma iye kucokera m'cigwa ca Hebroni, ndipo anadza ku Sekemu.

Werengani mutu wathunthu Genesis 37

Onani Genesis 37:14 nkhani