Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 37:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye anafotokozera atate wace ndi abale ace; ndipo atate wace anamdzudzula, nati kwa iye, Loto limene walota iwe nlotani? Kodi ine ndi amai ako ndi abale ako tidzafika ndithu tokha kuweramira iwe pansi?

Werengani mutu wathunthu Genesis 37

Onani Genesis 37:10 nkhani