Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 36:41-43 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

41. mfumu Oholibama, mfumu Ela, mfumu Pinoni;

42. mfumu Kenazi, mfumu Temani, mfumu Mibezari;

43. mfumu Magidieli, mfumu Iramu; amenewa ndi mafumu a Edomu, monga mwa kukhala kwao m'dziko lokhala laolao. Uyo ndiye Esau atate wao wa Aedomu.

Werengani mutu wathunthu Genesis 36